AKUNJOYA MA SCORCHERS

21 Aug 2026

Atsikana a timu ya Scorchers akuyendamchisangalalo pamene ma kampani akupitirira kumva kukoma pamene zabwino sizikuti leke. Atavinitsidwa ndi oimba Eli Njuchi komanso Tay Gryn, atsikanawa alandira ma set a kanema a DSTV kuchokera ku Multichoice Malawi. Izi zikudza pamene atsikanawa athera pa nambala yachiwiri mu mpikisano wa WAFCON 2026 umene umachirikira msziko la Morocco.

← Back to News