PARLIAMENT IFUFUZA MPUNGWEPUNGWE KU BT WATER BOARD
02 Sep 2026Sipikala wanyumba ya malamulo Sameer Suleiman wati makomiti ake apadera fufuza za kusamvana komwe kulipo ku bungwe logawa madzi la Blantyre Water Board, BWB. Poyankhula pa msonkhano wa atolankhani lachitatu pa 2 September chaka chino, Suleiman wati nyumba ya malamulo yalandira madandaulo kuchokera ku bungwe logawa madzi'li ndipo ati achita kanthu.
FULL STORY